Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova adzakumenyerani nkhondo,+ ndipo inu mudzakhala chete, osachitapo kalikonse.”

  • Ekisodo 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Yehova ndi wankhondo.+ Dzina lake ndi Yehova.+

  • Numeri 21:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Tsopano Yehova analankhula ndi Mose kuti: “Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake.+ Umuchite zimene unachitira Sihoni mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.”+

  • Deuteronomo 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+

  • Deuteronomo 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+

  • Yoswa 10:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Yoswa anagwira mafumu onsewa n’kulanda malo awo pa nthawi imodzi,+ chifukwa Yehova Mulungu wa Isiraeli ndiye anali kuwamenyera nkhondo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena