Ekisodo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo. Yesaya 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+
3 Ndinali kuonekera kwa Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo+ monga Mulungu Wamphamvuyonse.+ Koma za dzina langa lakuti Yehova,+ ine sindinadzidziwikitse+ kwa iwo.
8 “Ine ndine Yehova. Dzina langa ndi limeneli,+ ndipo sindidzapereka ulemu wanga kwa wina aliyense+ kapena kupereka ulemerero wanga+ kwa zifaniziro zogoba.+