Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndachita zimenezi kuti mufotokozere ana anu, ndi ana a ana anu, mmene ndakhaulitsira Iguputo ndi zizindikiro zimene ndachitira Aiguputo.+ Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+

  • Salimo 83:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+

      Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+

  • Luka 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo iye anawauza kuti: “Mukamapemphera+ muzinena kuti, ‘Atate, dzina lanu liyeretsedwe.+ Ufumu wanu ubwere.+

  • Yohane 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Atate lemekezani dzina lanu.” Pamenepo mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+

  • Machitidwe 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+

  • Chivumbulutso 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti:

      “Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena