Yesaya 55:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe udzaitana mtundu umene sukuudziwa,+ ndipo anthu a mtundu wosakudziwa adzathamangira kwa iwe+ chifukwa cha Yehova Mulungu wako,+ ndiponso chifukwa cha Woyera wa Isiraeli,+ pakuti iye adzakukongoletsa.+ 1 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+
5 Iwe udzaitana mtundu umene sukuudziwa,+ ndipo anthu a mtundu wosakudziwa adzathamangira kwa iwe+ chifukwa cha Yehova Mulungu wako,+ ndiponso chifukwa cha Woyera wa Isiraeli,+ pakuti iye adzakukongoletsa.+
9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+