Genesis 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anaonekera+ kwa Abulahamu pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure.+ Pa nthawiyi n’kuti Abulahamu atakhala pansi pakhomo la hema wake masana dzuwa likutentha.+
18 Kenako Yehova anaonekera+ kwa Abulahamu pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure.+ Pa nthawiyi n’kuti Abulahamu atakhala pansi pakhomo la hema wake masana dzuwa likutentha.+