Genesis 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+ Oweruza 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mngelo wa Yehova uja sanaonekerenso kwa Manowa ndi mkazi wake. Pamenepo Manowa anadziwa kuti anali mngelo wa Yehova.+ Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
7 Pambuyo pake, mngelo wa Yehova+ anakapeza Hagara m’chipululu ali pakasupe wamadzi wa panjira yopita ku Shura.+
21 Mngelo wa Yehova uja sanaonekerenso kwa Manowa ndi mkazi wake. Pamenepo Manowa anadziwa kuti anali mngelo wa Yehova.+
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+