Deuteronomo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake. Umuchite zimene unachitira Sihoni+ mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.’ Deuteronomo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna inu, musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo.’+ Deuteronomo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+
2 Chotero Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake. Umuchite zimene unachitira Sihoni+ mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.’
3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+