Deuteronomo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi amene akukumenyerani nkhondo.’+