Deuteronomo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna inu, musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo.’+