Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+ Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+
27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+
24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+