Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Atangowatulutsa mafumuwo anapita nawo kwa Yoswa. Iye anaitana amuna onse a Isiraeli amene anapita naye kunkhondoko, n’kuuza atsogoleri awo kuti: “Bwerani kuno muponde kumbuyo kwa makosi a mafumuwa.”+ Iwo anabwera n’kupondadi kumbuyo kwa makosi awo.+

  • Yoswa 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano awa ndi mafumu amene ana a Isiraeli anagonjetsa n’kulanda madera awo, kumbali yotulukira dzuwa+ ya mtsinje wa Yorodano. Analanda kuchokera kuchigwa* cha Arinoni+ kukafika kuphiri la Herimoni+ ndi ku Araba+ konse, kumbali yotulukira dzuwa. Mafumu ake ndi awa:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena