Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ 2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+ Salimo 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+
41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
40 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+