Yoswa 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atangowatulutsa mafumuwo anapita nawo kwa Yoswa. Iye anaitana amuna onse a Isiraeli amene anapita naye kunkhondoko, n’kuuza atsogoleri awo kuti: “Bwerani kuno muponde kumbuyo kwa makosi a mafumuwa.”+ Iwo anabwera n’kupondadi kumbuyo kwa makosi awo.+ Oweruza 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.” 2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+
24 Atangowatulutsa mafumuwo anapita nawo kwa Yoswa. Iye anaitana amuna onse a Isiraeli amene anapita naye kunkhondoko, n’kuuza atsogoleri awo kuti: “Bwerani kuno muponde kumbuyo kwa makosi a mafumuwa.”+ Iwo anabwera n’kupondadi kumbuyo kwa makosi awo.+
2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.”
41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+