2 Samueli 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+ Salimo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.+Dzanja lanu lamanja lidzapeza odana nanu. Salimo 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masoka adzapha munthu woipa.+Ndipo wodana ndi munthu wolungama adzapezeka wolakwa.+
41 Koma mudzachititsa adani anga kugonja* pamaso panga,+Anthu odana nane kwambiri, ndidzawakhalitsa chete.+