Salimo 94:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+ Yesaya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+
23 Iye adzawabwezera zoipa zawo,+Ndipo adzawakhalitsa chete mwa kuwadzetsera masoka okonza okha.+Yehova Mulungu wathu adzawakhalitsa chete.+
11 Tsoka kwa anthu oipa! Iwo adzaona zoopsa, chifukwa zimene anachitira ena ndi manja awo, zidzawachitikira iwowo.+