Genesis 43:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndikhala chikole cha moyo wa mnyamatayu.+ Chilangocho chikabwere pa ine.+ Ndikadzalephera kubwera naye ndi kum’pereka kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu moyo wanga wonse. Genesis 46:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yakobo anatumiza Yuda+ kuti atsogole kupita kwa Yosefe kukam’dziwitsa za kubwera kwa bambo ake ku Goseni. Pambuyo pake iwo anafika ku Goseni.+ 1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+
9 Ineyo ndikhala chikole cha moyo wa mnyamatayu.+ Chilangocho chikabwere pa ine.+ Ndikadzalephera kubwera naye ndi kum’pereka kwa inu, ndidzakhale wochimwa kwa inu moyo wanga wonse.
28 Yakobo anatumiza Yuda+ kuti atsogole kupita kwa Yosefe kukam’dziwitsa za kubwera kwa bambo ake ku Goseni. Pambuyo pake iwo anafika ku Goseni.+
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+