Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+ 2 Mbiri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mantha+ ochokera kwa Mulungu anagwira mafumu onse a m’dzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli.+
30 Yehova Mulungu wanu ndiye akukutsogolerani. Adzakumenyerani nkhondo+ mofanana ndi zonse zimene anakuchitirani ku Iguputo inu mukuona,+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+
29 Mantha+ ochokera kwa Mulungu anagwira mafumu onse a m’dzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli.+