Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo.

  • 2 Mbiri 14:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kuwonjezera apo, anawononga mizinda yonse yozungulira Gerari chifukwa mantha+ ochokera kwa Yehova anagwira anthu a m’mizindayo. Iwo anafunkha mizinda yonseyo, chifukwa munali zambiri zoti afunkhe.+

  • 2 Mbiri 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mantha+ ochokera kwa Yehova anagwira maufumu onse a m’mayiko ozungulira Yuda, ndipo sanachite nkhondo ndi Yehosafati.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena