Genesis 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo. Deuteronomo 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibe munthu amene adzaima kuti alimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzapondapo kugwidwa ndi mantha aakulu ndi kukuopani,+ monga mmene anakulonjezerani.
5 Atatero anachoka, ndipo anthu a m’mizinda yowazungulira anagwidwa ndi mantha ochokera kwa Mulungu,+ moti sanatsatire ana a Yakobo kuti akawathire nkhondo.
25 Palibe munthu amene adzaima kuti alimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzapondapo kugwidwa ndi mantha aakulu ndi kukuopani,+ monga mmene anakulonjezerani.