Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzatekeseka.+Okhala ku Filisitiya adzamva zopweteka ngati za pobereka.+ Deuteronomo 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+ Yoswa 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anamuyankha kuti: “Akapolo anufe tachokera kudziko lakutali kwambiri.+ Tabwera chifukwa tamva za dzina+ la Mulungu wanu, Yehova. Tamva mbiri yake ndi zonse zimene anachita ku Iguputo.+
26 Palibe wina wofanana ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda m’mlengalenga pokuthandiza,+Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+
9 Iwo anamuyankha kuti: “Akapolo anufe tachokera kudziko lakutali kwambiri.+ Tabwera chifukwa tamva za dzina+ la Mulungu wanu, Yehova. Tamva mbiri yake ndi zonse zimene anachita ku Iguputo.+