1 Mafumu 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Komanso mlendo+ amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu+ 2 Mbiri 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Komanso mlendo amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli,+ amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu lalikulu,+ ndi dzanja lanu lamphamvu+ ndi mkono wanu wotambasuka,+ ndipo iwo abwera n’kupemphera atayang’ana nyumba ino,+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+
41 “Komanso mlendo+ amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli, amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu+
32 “Komanso mlendo amene sali mmodzi wa anthu anu Aisiraeli,+ amene wabwera kuchokera kudziko lakutali chifukwa cha dzina lanu lalikulu,+ ndi dzanja lanu lamphamvu+ ndi mkono wanu wotambasuka,+ ndipo iwo abwera n’kupemphera atayang’ana nyumba ino,+