Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ngati mlendo wokhala nanu akufuna kuchita nanu chikondwerero cha pasika kwa Yehova, mwamuna aliyense wa m’nyumba yake adulidwe.+ Akatero atha kuchita nawo chikondwererocho, ndipo ayenera kuonedwa ngati mbadwa ya dzikolo. Koma munthu wosadulidwa asadye nawo.

  • Rute 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Rute anati: “Musandichonderere kuti ndikusiyeni, kuti ndibwerere ndisakutsatireni, pakuti kumene inu mupite inenso ndipita komweko, kumene inu mugone inenso ndigona komweko.+ Anthu a mtundu wanu adzakhala anthu a mtundu wanga,+ ndipo Mulungu wanu adzakhala Mulungu wanga.+

  • Yesaya 56:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mlendo yemwe wadziphatika kwa Yehova asanene kuti,+ ‘Ndithu Yehova adzandilekanitsa ndi anthu ake.’+ Nayenso munthu wofulidwa+ asanene kuti, ‘Ine ndiye ndine mtengo wouma basi.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena