Genesis 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ m’mibadwo yanu yonse. Aliyense wobadwira m’nyumba yanu ndi aliyense wosakhala mbewu yanu koma wogulidwa ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.
12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ m’mibadwo yanu yonse. Aliyense wobadwira m’nyumba yanu ndi aliyense wosakhala mbewu yanu koma wogulidwa ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.