Machitidwe 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pali anthu ochokera ku Fulugiya,+ ku Pamfuliya,+ ku Iguputo ndi kumadera a Libiya amene ali kufupi ndi Kurene. Palinso alendo ochokera ku Roma, amene ndi Ayuda ndi otembenukira ku Chiyuda,+
10 Pali anthu ochokera ku Fulugiya,+ ku Pamfuliya,+ ku Iguputo ndi kumadera a Libiya amene ali kufupi ndi Kurene. Palinso alendo ochokera ku Roma, amene ndi Ayuda ndi otembenukira ku Chiyuda,+