Machitidwe 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano amunawo, pamodzi ndi Paulo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anafika ku Pega, ku Pamfuliya.+ Koma Yohane+ anawasiya ndi kubwerera+ ku Yerusalemu. Machitidwe 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Paulo anaona kuti n’kosayenera kumutenga kuti apite nawo. Anaona kuti n’kosayenera chifukwa ulendo wapita Yohane anawasiya ku Pamfuliya+ ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.
13 Tsopano amunawo, pamodzi ndi Paulo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anafika ku Pega, ku Pamfuliya.+ Koma Yohane+ anawasiya ndi kubwerera+ ku Yerusalemu.
38 Koma Paulo anaona kuti n’kosayenera kumutenga kuti apite nawo. Anaona kuti n’kosayenera chifukwa ulendo wapita Yohane anawasiya ku Pamfuliya+ ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.