Machitidwe 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Paulo anaona kuti si bwino kumutenga chifukwa ulendo wina Yohane anawasiya ku Pamfuliya ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:38 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 8
38 Koma Paulo anaona kuti si bwino kumutenga chifukwa ulendo wina Yohane anawasiya ku Pamfuliya ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.+