Machitidwe 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Paulo anaona kuti n’kosayenera kumutenga kuti apite nawo. Anaona kuti n’kosayenera chifukwa ulendo wapita Yohane anawasiya ku Pamfuliya+ ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:38 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 8
38 Koma Paulo anaona kuti n’kosayenera kumutenga kuti apite nawo. Anaona kuti n’kosayenera chifukwa ulendo wapita Yohane anawasiya ku Pamfuliya+ ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.