Deuteronomo 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Palibe amene angafanane ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda mumlengalenga kuti akuthandize,Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+
26 Palibe amene angafanane ndi Mulungu woona+ wa Yesuruni,+Amene amayenda mumlengalenga kuti akuthandize,Amene amayenda pamitambo mu ulemerero wake.+