Salimo 109:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndithandizeni, inu Yehova Mulungu wanga.+Ndipulumutseni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+ Mateyu 27:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+ 1 Timoteyo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa chifukwa chimenechi, tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo+ chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi+ wa anthu a mtundu uliwonse,+ koma makamaka okhulupirika.+
43 Suja amakhulupirira Mulungu? Mulunguyo am’pulumutse+ tsopano ngati akumufunadi. Ndi ujatu anali kunena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+
10 Pa chifukwa chimenechi, tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo+ chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi+ wa anthu a mtundu uliwonse,+ koma makamaka okhulupirika.+