Salimo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khalani wofunitsitsa kundilanditsa, inu Yehova.+Inu Yehova, fulumirani kundithandiza.+ Salimo 119:86 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 86 Malamulo anu onse ndi odalirika.+Odzikuza andizunza popanda chifukwa. Chonde, ndithandizeni.+