Salimo 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+ Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+
19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+
6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+