1 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.” Salimo 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+ Salimo 119:154 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 154 Ndiyankhireni mlandu wanga ndi kundipulumutsa.+Ndisungeni wamoyo mogwirizana ndi mawu anu.+
15 Yehova akhale woweruza, ndipo aweruze pakati pa ine ndi inu. Iye adzandiweruzira mlanduwu+ ndi kuchitapo kanthu kuti andimasule m’manja mwanu.”
43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+