Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 19:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 kuti musakhetse magazi a munthu wosalakwa+ pakati pa dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, kotero kuti musakhale ndi mlandu wa magazi.+

  • 1 Samueli 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Tsopano mbuyanga, ndikulumbira pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ komanso pali moyo wanu:+ Yehova wakubwezani+ kuti musapalamule mlandu wamagazi+ komanso kuti musadzipulumutse nokha ndi dzanja lanu.+ Choncho lolani kuti adani anu ndi onse ofuna kukuvulazani mbuyanga, akhale ngati Nabala.+

  • Salimo 73:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Koma ine phazi langa linangotsala pang’ono kupatuka,+

      Mapazi anga anangotsala pang’ono kuterereka.+

  • Miyambo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+

  • Yakobo 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena