Genesis 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+ Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+
6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+