Miyambo 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+ 1 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano pa nkhani imene munalemba ija, ndi bwino kuti mwamuna asakhudze+ mkazi.
29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+