Genesis 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+ Deuteronomo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+ Miyambo 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+
6 Pamenepo Mulungu woona anamuuza m’malotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi,+ ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire.+ Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.+
28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+
29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+