Genesis 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano Yakobo anamva zakuti Sekemu wagwiririra mwana wake Dina. Pa nthawiyo n’kuti ana ake aamuna ali kubusa ndi ziweto zake.+ Choncho, Yakobo sananene kanthu kudikira kuti ana akewo abwere.+ Ekisodo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Mwamuna akanyengerera namwali wosalonjezedwa kukwatiwa n’kugona naye,+ azim’tenga ndithu kukhala mkazi wake atapereka chiwongo.*+
5 Tsopano Yakobo anamva zakuti Sekemu wagwiririra mwana wake Dina. Pa nthawiyo n’kuti ana ake aamuna ali kubusa ndi ziweto zake.+ Choncho, Yakobo sananene kanthu kudikira kuti ana akewo abwere.+
16 “Mwamuna akanyengerera namwali wosalonjezedwa kukwatiwa n’kugona naye,+ azim’tenga ndithu kukhala mkazi wake atapereka chiwongo.*+