Genesis 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake, Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Kodi abale ako sakudyetsa nkhosa cha ku Sekemu? Tabwera ndikutume kwa iwo.” Iye anati: “Chabwino bambo.”+
13 Pambuyo pake, Isiraeli anauza Yosefe kuti: “Kodi abale ako sakudyetsa nkhosa cha ku Sekemu? Tabwera ndikutume kwa iwo.” Iye anati: “Chabwino bambo.”+