Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+ Deuteronomo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+
2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+
28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+