Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+ 2 Samueli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Aminoni sanamvere mawu ake. Popeza anali ndi mphamvu zoposa Tamara, anamuchititsa manyazi+ mwa kugona naye.+
2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+
14 Koma Aminoni sanamvere mawu ake. Popeza anali ndi mphamvu zoposa Tamara, anamuchititsa manyazi+ mwa kugona naye.+