Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno ana a Mulungu+ woona anayamba kuona+ kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Chotero, anayamba kudzitengera okha akazi alionse amene anawasankha.

  • Genesis 34:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anaphanso Hamori ndi mwana wake Sekemu ndi lupanga.+ Kenako anatenga Dina m’nyumba ya Sekemu, n’kupita naye.+

  • Deuteronomo 22:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 mwamunayo azipereka masekeli 50 asiliva kwa bambo a mtsikanayo,+ ndipo akhale mkazi wake chifukwa chakuti wamunyazitsa. Sadzaloledwa kumusiya ukwati masiku onse a moyo wake.+

  • 2 Samueli 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma Aminoni sanamvere mawu ake. Popeza anali ndi mphamvu zoposa Tamara, anamuchititsa manyazi+ mwa kugona naye.+

  • 1 Akorinto 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena