Yobu 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Ndachita pangano ndi maso anga.+Choncho ndingayang’anitsitse bwanji namwali?+ Yakobo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa mwa kukopedwa ndi kukodwa m’chilakolako chake.+