Yobu 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati mtima wanga wakopeka ndi mkazi,+Ndipo ndinali kudikirira+ pakhomo lolowera kunyumba kwa mnzanga, 1 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano pa nkhani imene munalemba ija, ndi bwino kuti mwamuna asakhudze+ mkazi.
9 Ngati mtima wanga wakopeka ndi mkazi,+Ndipo ndinali kudikirira+ pakhomo lolowera kunyumba kwa mnzanga, 1 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano pa nkhani imene munalemba ija, ndi bwino kuti mwamuna asakhudze+ mkazi.