Yobu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake.
15 Diso la wachigololo+ limadikira kuti mdima ugwe madzulo.+Iye amati, ‘Palibe diso limene lindione,’+Ndipo amaphimba kumaso kwake.