2 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iweyo unachita zinthu zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzachita zimenezi pamaso pa Isiraeli+ yense, masanasana.’”+ Salimo 94:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amanena kuti: “Ya sakuona,+Ndipo Mulungu wa Yakobo sakudziwa zimene zikuchitika.”+ Miyambo 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nayi njira ya mkazi wachigololo: Iye amadya n’kupukuta pakamwa pake ndipo amanena kuti: “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+
12 Iweyo unachita zinthu zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzachita zimenezi pamaso pa Isiraeli+ yense, masanasana.’”+
20 Nayi njira ya mkazi wachigololo: Iye amadya n’kupukuta pakamwa pake ndipo amanena kuti: “Sindinachite cholakwa chilichonse.”+