Mateyu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ Luka 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komatu palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndi chinsinsi chimene sichidzadziwika.+
26 Choncho musawaope, pakuti palibe chobisika chimene sichidzaululika, ndipo palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+