Luka 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komatu palibe chimene chabisidwa mwachinsinsi kwambiri chimene sichidzaululika komanso palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 180 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 8
2 Komatu palibe chimene chabisidwa mwachinsinsi kwambiri chimene sichidzaululika komanso palibe chinsinsi chimene sichidzadziwika.+