Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti chilichonse chobisidwa chidzaululika. Chilichonse chimene chimasungidwa mwachinsinsi kwambiri chidzadziwika.+

  • Luka 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chilichonse chobisidwa+ chidzaonekera poyera. Ndipo zinthu zonse zosungidwa mwachinsinsi kwambiri zidzadziwika ndi kuululika.+

  • 1 Akorinto 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero musaweruze+ kalikonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike.+ Akadzafika adzaunika zinsinsi za mu mdima+ ndi kuonetsa poyera+ zolingalira za m’mitima, ndipo aliyense adzatamandidwa yekha ndi Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena