Deuteronomo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngati mwamuna wakumana ndi namwali amene sanalonjezedwe ndi mwamuna kuti adzamukwatira ndipo wamugwira nʼkugona naye, ndiyeno agwidwa,+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:28 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 31
28 Ngati mwamuna wakumana ndi namwali amene sanalonjezedwe ndi mwamuna kuti adzamukwatira ndipo wamugwira nʼkugona naye, ndiyeno agwidwa,+