Deuteronomo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:28 Nsanja ya Olonda,11/15/1989, tsa. 31
28 “Mwamuna akapeza ndi kugwira mtsikana, namwali wosalonjezedwa kukwatiwa, n’kugona naye+ ndipo onsewo agwidwa,+